Njuchi
(Sispence on the board)
Ooh, yeah

These were the words he said
Tili mu deport ndisananyamuke
Ukadutsa Dedza, dzayimbe phone
Let me know if you're gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone
Ayi mwanawe basi ndiye kadzipita
Akumakwera usayang'ane m'mbuyo
Zikakayenda kwinako don't forget where you're coming from

Dzayimbe phone
Let me know if you're gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone

Ukakafika dzandiyimbilе
Map ndzakulondolere
Ukakafika dzandiyimbile
Incasе ungadzaponde ndele
Nthawi yomweyi, mwakula nsanga
Oh, I'm gonna miss you Chifu'
Mwana wanga moyo ngosavuta kwa okhawo odziwa Chauta
Zikakafika povuta mvera nkuwuze chokachita

Dzayimbe phone
Anytime when you feel like you're lonely
Dzayimbe phone
Tidzakhale pansi tidzakochane
Ndati, dzayimbe phone
Let me know if you're gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone

Mukunkako chonde kumakalimbika
Kumakalimba zinthu zikamakafoka
Osasintha mtima omadzichepetsa
Tizibwana tingapo kumadziletsa

Zikakavuta dzatiyimbile
Za WhatsApp ife ndikumanzele
Mamuna samadzipatsa malire
Sizoti kungokwiya basi mupakile
Tili kuno tikudikira
Ndipo kwathu ndikuyamikila
A Eli Njuchi ndithudi mwakula
Nambala ndiyo zikamakakula

Dzayimbe phone
Anytime when you feel like you're lonely
Dzayimbe phone
Tidzakhale pansi tidzakochane
Ndati, dzayimbe phone
Let me know if you're gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone

Dzayimbe phone, ih, oh-yeah
Dzayimbe phone, ih, oh-yeah
Dzayimbe phone, ni, oh-yeah
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone

Ndikafika pothodwa ndithudi ndimayimba phone
And then he tells me "son osagonja"
Usawapatse chokamba ana
Usakondweretse mdani
Ukamagona yimba phone
Kwa Namalenga ndizotheka, imba phone

Dzayimbe phone
Anytime when you feel like you're lonely
Dzayimbe phone
Tidzakhale pansi tidzakochane
Ndati, dzayimbe phone
Let me know if you're gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone

Zikadzavuta ndati dzayimbe phone
Ndati zikadzavuta ndithu dzayimbe phone
Zikadzavuta ndati dzayimbe phone
Ndati zikadzavuta ndithu dzayimbe phone
Zikadzavuta mwana dzayimbe phone
Ndati zikadzavuta mwana dzayimbe phone
Zikadzavuta mwana dzayimbe phone
Moti zikadzavuta mwana dzayimbe phone

Comments (0)