Moyo ndi ulendo
Kutali tayenda limo-
Kudziwa umkadziwa
Kuti idzakwana nthawi
Tidzayenda njira zosiyana
Maria-Maria, ndayimba nyimbo utonthole
Maria-Maria, ndilinawe usayiwale
Maria-Maria, ndayimba nyimbo utonthole
Maria-Maria, ndilinawe usayiwale
Njira watengayo dziwa ili m'thengo
Ulendo wayambawo uvale zilimbe
Uye, uvale zilimbe
Namalenga adzakudalitsa ndi mphamvu
Chonde usamangike
Mwana wane dziwa ndiwe mfulu
You can be whoever you want
Pagulu udzichepetse iwe
Dziwa uli ku nkhondo
Nkhondo uyimalize
As I am singing this song
Ndili pambalipo Maria
Chonde umwetulire
Usiye kulira Maria
Maria-Maria, ndayimba nyimbo utonthole
Maria-Maria, ndilinawe usayiwale
Maria-Maria, ndayimba nyimbo utonthole
Maria-Maria, ndilinawe usayiwale
Maria-Maria, Maria-Maria
Maria-Maria, Maria-Maria
Maria-Maria, Maria-Maria
Maria-Maria, Maria-Maria
Ooh, msamaleni
Achibale msamaleni
Ngati wanu mkuzeni
Ku dziko mtetezeni
Oh, mphuzitseni
Achibale mphuzitseni
Ngati wanu mkondeni
Mtetezeni, aah
Maria-Maria, (Maria-Maria)
Maria-Maria, (Maria-Maria)
Maria-Maria, nkhukutemwa chomene
Maria-Maria, (Maria-Maria)
Maria-Maria, (Maria)
Nawakwitu (nawakwitu-nawakwitu-nawakwitu)
Comments (0)