Ooh yeah yeah
Njuchi

Inali nyimbo yosapekedwa
Inali nyimbo yosadziwidwa
Sindidapemphe kuti mundilembe
Sindidapemphe kuti ndiyimbidwe
Nditayimbidwa kumene
Mudanditama achimwene
Ndithu nditayimbidwa kumene
Munandigawa achimwene
Kumpoto, kum'mwela, pakati
Konseku ndinali mkamwa mwawo
Amkandikonda amkandivina
Ah yeah ndikati ndiyambe

Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Sindinapemphe kuti mundilembe
Sinnapemphe kuti ndiyimbidwe
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Sindinapemphe napemphe napemphe
Napemphe napemphe
Ooh yeah
Ooh yeah

Ooh yeah yeah
Ndinali mphatso m'moyo mwawo
Chimwemwe m'mitima yawo ooh
They used to say i was a hit on the radio
Number one on every chat list aah eeh
Pangopita nthawi
Olo ndi chaka sichinakwane
Zoti ndine ndemwe n'nali pa repeat
Ndikumadya next abo bii delete
Yakwana, yafwifwa
Yapola moto
Tidzichewa towawa mkwamwa mwawo
Amkandikonda amkandivina
Ah yeah ndikati ndiyambe

Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Sindinapemphe kuti mundilembe
Sinnapemphe kuti ndiyimbidwe
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Sindinapemphe napemphe napemphe
Napemphe napemphe

Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Sindinapemphe kuti mundilembe
Sinnapemphe kuti ndiyimbidwe
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Uuu yeah yeah yeah yeah nyimbo
Sindinapemphe napemphe napemphe
Napemphe napemphe
Ooh yeah

Zili ngati banjalo
Sindinapemphe kuti ndiyimbidwe
Abambo a Junior
Sindinapemphe kuti ndiyimbidwe
Nkhani zachikondizi
Sindinapemphe kuti ndiyimbidwe
Sindinapemphe ine
Sindinapemphe

Ih-yo yeah ay yah yah
Ooh ih-yo yeah ay yah yah
Sispense iwe
Ih-yo yeah ay yah yah
Njuchi iwe
Ih-yo yeah ay yah yah

Comments (0)